-
2 Mbiri 35:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Pamenepo Neko anatumiza anthu kwa iye kukamuuza kuti: “Kodi ndili nawe chiyani iwe mfumu ya Yuda? Lero sindinabwere kudzamenyana ndi iweyo. Ndabwera kudzamenyana ndi mtundu wina umene Mulungu wanena kuti ndikauwopseze. Ngati ukufuna kuti zinthu zikuyendere bwino, usachite zimenezi. Uope Mulungu amene ali nane ndipo usalole kuti iye akuwononge.”+
-