25 Yeremiya+ anayamba kuimbira Yosiya nyimbo ya maliro.+ Oimba onse aamuna ndi aakazi+ amanenabe za Yosiya m’nyimbo zawo zoimba polira mpaka lero. Nyimbo zimenezi zinakhazikitsidwa ngati lamulo mu Isiraeli, ndipo zinalembedwa m’nyimbo zoimba polira.+