Ezara 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Aliyense amene akukhala monga mlendo+ kumalo alionse, anthu akwawo amuthandize ndi siliva, golide, katundu, ziweto, limodzi ndi nsembe yaufulu+ ya nyumba ya Mulungu woona, yomwe inali ku Yerusalemu.’”
4 Aliyense amene akukhala monga mlendo+ kumalo alionse, anthu akwawo amuthandize ndi siliva, golide, katundu, ziweto, limodzi ndi nsembe yaufulu+ ya nyumba ya Mulungu woona, yomwe inali ku Yerusalemu.’”