Ezara 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kuyambira pa tsiku loyamba la mwezi wa 7+ kupita m’tsogolo, anthuwo anayamba kupereka nsembe zopsereza kwa Yehova. Pa nthawiyi n’kuti maziko a kachisi wa Yehova asanamangidwe. Ezara Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:6 Nsanja ya Olonda,1/15/2006, tsa. 19
6 Kuyambira pa tsiku loyamba la mwezi wa 7+ kupita m’tsogolo, anthuwo anayamba kupereka nsembe zopsereza kwa Yehova. Pa nthawiyi n’kuti maziko a kachisi wa Yehova asanamangidwe.