Ezara 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma chifukwa chakuti makolo athu anakwiyitsa+ Mulungu wakumwamba, iye anawapereka+ m’manja mwa Nebukadinezara+ mfumu ya Babulo Mkasidi,+ yemwe anagwetsa nyumbayi+ n’kutengera anthuwo ku ukapolo ku Babulo.+
12 Koma chifukwa chakuti makolo athu anakwiyitsa+ Mulungu wakumwamba, iye anawapereka+ m’manja mwa Nebukadinezara+ mfumu ya Babulo Mkasidi,+ yemwe anagwetsa nyumbayi+ n’kutengera anthuwo ku ukapolo ku Babulo.+