Ezara 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anthu ochokera pa ana a Adonikamu+ omwe anali omaliza, mayina awo anali awa: Elifeleti, Yeyeli ndi Semaya. Iwo anali ndi amuna 60.
13 Anthu ochokera pa ana a Adonikamu+ omwe anali omaliza, mayina awo anali awa: Elifeleti, Yeyeli ndi Semaya. Iwo anali ndi amuna 60.