Ezara 8:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Pomalizira pake tinachoka pamtsinje wa Ahava+ pa tsiku la 12 la mwezi woyamba+ kuti tipite ku Yerusalemu. Dzanja la Mulungu wathu linali nafe pa ulendowu moti anatipulumutsa+ m’manja mwa adani ndiponso kwa achifwamba a m’njira.
31 Pomalizira pake tinachoka pamtsinje wa Ahava+ pa tsiku la 12 la mwezi woyamba+ kuti tipite ku Yerusalemu. Dzanja la Mulungu wathu linali nafe pa ulendowu moti anatipulumutsa+ m’manja mwa adani ndiponso kwa achifwamba a m’njira.