12 Ndiyeno ndinadzuka usiku pamodzi ndi amuna angapo amene ndinali nawo. Sindinauze munthu aliyense+ zimene Mulungu wanga anali kuika mumtima mwanga zoti ndichitire Yerusalemu,+ ndipo ndinalibe chiweto chilichonse kupatulapo chiweto chimene ndinakwerapo.