16 Ndiyeno Nehemiya mwana wamwamuna wa Azibuki, kalonga wa hafu ya chigawo cha Beti-zuri,+ anakonza mpandawo kuchokera pamene Saluni analekezera, kukafika patsogolo pa Manda Achifumu+ a Davide ndi kudziwe+ lochita kukumba, mpaka kukafikanso ku Nyumba ya Anthu Amphamvu.+