17 Ndiyeno Alevi,+ moyang’aniridwa ndi Rehumu mwana wamwamuna wa Bani,+ anakonza mpandawo kuchokera pamene Nehemiya analekezera. Hasabiya, kalonga wa hafu ya chigawo cha Keila,+ anakonza mpanda kuimira chigawo chake kuchokera pamene Alevi analekezera.