Nehemiya 3:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kenako, Atekowa+ anakonza chigawo chinanso cha mpandawo, kuchokera patsogolo pa nsanja yaikulu yotundumukira kunja kwa mpanda ija mpaka kukafika kumpanda wa Ofeli.
27 Kenako, Atekowa+ anakonza chigawo chinanso cha mpandawo, kuchokera patsogolo pa nsanja yaikulu yotundumukira kunja kwa mpanda ija mpaka kukafika kumpanda wa Ofeli.