Nehemiya 4:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma ine,+ abale anga,+ atumiki anga+ ndi amuna olondera+ amene anali pambuyo panga, sitinali kuvula zovala zathu, ndipo aliyense anali ndi mkondo+ m’dzanja lake lamanja.
23 Koma ine,+ abale anga,+ atumiki anga+ ndi amuna olondera+ amene anali pambuyo panga, sitinali kuvula zovala zathu, ndipo aliyense anali ndi mkondo+ m’dzanja lake lamanja.