Nehemiya 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno ndinati: “Zimene mukuchitazi si zabwino ayi.+ Kodi simuyenera kuyenda moopa+ Mulungu+ kuti tipewe chitonzo+ cha adani athu, anthu a mitundu ina?+
9 Ndiyeno ndinati: “Zimene mukuchitazi si zabwino ayi.+ Kodi simuyenera kuyenda moopa+ Mulungu+ kuti tipewe chitonzo+ cha adani athu, anthu a mitundu ina?+