Esitere 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 M’masiku amenewo, pamene Moredekai anali kukhala pansi kuchipata cha mfumu, Bigitana ndi Teresi, nduna ziwiri za panyumba ya mfumu, amenenso anali alonda a pakhomo, anakwiya ndipo anafuna kupha+ Mfumu Ahasiwero.
21 M’masiku amenewo, pamene Moredekai anali kukhala pansi kuchipata cha mfumu, Bigitana ndi Teresi, nduna ziwiri za panyumba ya mfumu, amenenso anali alonda a pakhomo, anakwiya ndipo anafuna kupha+ Mfumu Ahasiwero.