4 Pakuti ine ndi anthu a mtundu wanga tagulitsidwa+ kuti tiwonongedwe, tiphedwe ndi kufafanizidwa.+ Ngati tikanagulitsidwa kukhala akapolo aamuna+ ndi akapolo aakazi ndikanakhala chete. Koma musalole kuti tsoka limeneli lichitike chifukwa liwonongetsa zinthu zambiri za mfumu.”