Esitere 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Zimene analemba+ m’makalatawo anazipereka kuti zikhale lamulo m’zigawo zonse. Anazifalitsa kwa anthu a mitundu yonse kuti Ayuda akonzekere kudzabwezera+ adani awo pa tsiku limeneli. Esitere Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:13 Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu,3/2016, tsa. 3
13 Zimene analemba+ m’makalatawo anazipereka kuti zikhale lamulo m’zigawo zonse. Anazifalitsa kwa anthu a mitundu yonse kuti Ayuda akonzekere kudzabwezera+ adani awo pa tsiku limeneli.