Yobu 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kodi inuyo simwam’tchinga iyeyo?+ Mwatchingiranso nyumba yake ndi chilichonse chimene ali nacho. Mwadalitsa ntchito ya manja ake+ ndipo ziweto zake zachuluka kwambiri padziko lapansi. Yobu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:10 Nsanja ya Olonda,11/15/1994, tsa. 11 Kukhala ndi Moyo Kosatha, ptsa. 107-108
10 Kodi inuyo simwam’tchinga iyeyo?+ Mwatchingiranso nyumba yake ndi chilichonse chimene ali nacho. Mwadalitsa ntchito ya manja ake+ ndipo ziweto zake zachuluka kwambiri padziko lapansi.