Yobu 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Atakweza maso awo ali chapatali, sanamuzindikire poyamba. Kenako anayamba kulira mokweza mawu ndipo aliyense anang’amba+ malaya ake akunja odula manja, n’kuwaza fumbi m’mwamba pamwamba pa mitu yawo.+
12 Atakweza maso awo ali chapatali, sanamuzindikire poyamba. Kenako anayamba kulira mokweza mawu ndipo aliyense anang’amba+ malaya ake akunja odula manja, n’kuwaza fumbi m’mwamba pamwamba pa mitu yawo.+