Yobu 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kapena ndi akalonga amene ali ndi golide,Amene amadzaza nyumba zawo ndi siliva.