Yobu 19:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inetu ndakhala ndikukuwa kuti, ‘Chiwawa!’ koma palibe woyankha.+Ndakhala ndikufuula popempha thandizo, koma chilungamo sichikupezeka.+
7 Inetu ndakhala ndikukuwa kuti, ‘Chiwawa!’ koma palibe woyankha.+Ndakhala ndikufuula popempha thandizo, koma chilungamo sichikupezeka.+