Yobu 26:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Komatu zimenezi ndi kambali kakang’ono chabe ka zochita zake,+Ndipo timangomva kunong’ona kwapansipansi kwa mawu ake.Koma kodi mabingu ake amphamvu, angawamvetse ndani?”+
14 Komatu zimenezi ndi kambali kakang’ono chabe ka zochita zake,+Ndipo timangomva kunong’ona kwapansipansi kwa mawu ake.Koma kodi mabingu ake amphamvu, angawamvetse ndani?”+