Salimo 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Inu ana a anthu, kodi mudzandinyoza chifukwa cha ulemerero wanga+ kufikira liti?Mudzakonda zinthu zopanda pake kufikira liti?Mudzafunafuna nkhani yoti mundinamizire kufikira liti? [Seʹlah.] Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:2 Nsanja ya Olonda,5/15/2011, tsa. 31
2 Inu ana a anthu, kodi mudzandinyoza chifukwa cha ulemerero wanga+ kufikira liti?Mudzakonda zinthu zopanda pake kufikira liti?Mudzafunafuna nkhani yoti mundinamizire kufikira liti? [Seʹlah.]