Salimo 22:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Anthu onse a padziko lapansi onyada chifukwa cha chuma chawo adzadya ndi kuwerama.+Onse otsikira kufumbi adzawerama pamaso pake,+Ndipo palibe amene adzapulumutsa moyo wake.+
29 Anthu onse a padziko lapansi onyada chifukwa cha chuma chawo adzadya ndi kuwerama.+Onse otsikira kufumbi adzawerama pamaso pake,+Ndipo palibe amene adzapulumutsa moyo wake.+