Salimo 29:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Liwu la Yehova likuchititsa mbawala zazikazi kuphiriphitha ndi ululu wa pobereka,+Ndipo likufafaniza nkhalango.+M’kachisi wake aliyense akunena kuti: “Ulemerero ndi wa Mulungu!”+
9 Liwu la Yehova likuchititsa mbawala zazikazi kuphiriphitha ndi ululu wa pobereka,+Ndipo likufafaniza nkhalango.+M’kachisi wake aliyense akunena kuti: “Ulemerero ndi wa Mulungu!”+