Salimo 30:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndidzakutamandani inu Yehova, pakuti mwandipulumutsa,+Ndipo simunalole kuti adani anga akondwere ndi kusautsika kwanga.+
30 Ndidzakutamandani inu Yehova, pakuti mwandipulumutsa,+Ndipo simunalole kuti adani anga akondwere ndi kusautsika kwanga.+