Salimo 48:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Phiri la Ziyoni limene lili m’dera lakutali la kumpoto,+Ndi lokongola chifukwa lili pamalo okwezeka ndi osangalatsa padziko lonse lapansi,+Mudzi wa Mfumu Yaikulu.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 48:2 ‘Dziko Lokoma’, tsa. 20
2 Phiri la Ziyoni limene lili m’dera lakutali la kumpoto,+Ndi lokongola chifukwa lili pamalo okwezeka ndi osangalatsa padziko lonse lapansi,+Mudzi wa Mfumu Yaikulu.+