Salimo 68:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mafumu enieniwo okhala ndi magulu a asilikali amathawa, ndithu amathawadi.+Mkazi wongokhala pakhomo, nayenso amagwira nawo ntchito yofunkha.+
12 Mafumu enieniwo okhala ndi magulu a asilikali amathawa, ndithu amathawadi.+Mkazi wongokhala pakhomo, nayenso amagwira nawo ntchito yofunkha.+