Salimo 69:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mtima wanga wasweka chifukwa cha chitonzo, ndipo chilonda chake ndi chosachiritsika.+Ndinali kuyembekezera kuti wina andimvere chifundo, koma panalibe ndi mmodzi yemwe,+Ndinali kuyembekezera onditonthoza, koma sanapezeke ngakhale mmodzi.+
20 Mtima wanga wasweka chifukwa cha chitonzo, ndipo chilonda chake ndi chosachiritsika.+Ndinali kuyembekezera kuti wina andimvere chifundo, koma panalibe ndi mmodzi yemwe,+Ndinali kuyembekezera onditonthoza, koma sanapezeke ngakhale mmodzi.+