Salimo 85:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 85 Inu Yehova, mwasangalala ndi dziko lanu.+Mwabwezeretsa ana a Yakobo amene anagwidwa ndi kutengedwa kupita kudziko lina.+
85 Inu Yehova, mwasangalala ndi dziko lanu.+Mwabwezeretsa ana a Yakobo amene anagwidwa ndi kutengedwa kupita kudziko lina.+