Salimo 86:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ikani chizindikiro cha ubwino wanu pa ine,Kuti anthu odana nane aone zimenezi ndi kuchita manyazi,+Pakuti inu Yehova mwandithandiza ndi kundilimbikitsa.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 86:17 Nsanja ya Olonda,4/15/1993, tsa. 3112/15/1992, ptsa. 17-19
17 Ikani chizindikiro cha ubwino wanu pa ine,Kuti anthu odana nane aone zimenezi ndi kuchita manyazi,+Pakuti inu Yehova mwandithandiza ndi kundilimbikitsa.+