Salimo 88:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mkwiyo wanu wagwera pa ine,+Ndipo mwandisautsa ndi mafunde anu onse amphamvu.+ [Seʹlah.]