Salimo 88:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kodi anthu akufa mudzawachitira zodabwitsa?+Kapena kodi anthu akufa, anthu amene sangachite kanthu, adzauka?+Kodi adzakutamandani?+ [Seʹlah.]
10 Kodi anthu akufa mudzawachitira zodabwitsa?+Kapena kodi anthu akufa, anthu amene sangachite kanthu, adzauka?+Kodi adzakutamandani?+ [Seʹlah.]