Salimo 106:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Iwo anapanganso mwana wa ng’ombe ku Horebe,+Ndipo anaweramira chifaniziro chopangidwa ndi chitsulo chosungunula.+
19 Iwo anapanganso mwana wa ng’ombe ku Horebe,+Ndipo anaweramira chifaniziro chopangidwa ndi chitsulo chosungunula.+