Salimo 119:90 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 90 Kukhulupirika kwanu kudzakhalapobe ku mibadwomibadwo.+Mwakhazikitsa mwamphamvu dziko lapansi, kuti lisagwedezeke.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 119:90 Nsanja ya Olonda,4/15/2005, ptsa. 15-16
90 Kukhulupirika kwanu kudzakhalapobe ku mibadwomibadwo.+Mwakhazikitsa mwamphamvu dziko lapansi, kuti lisagwedezeke.+