Miyambo 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mkazi wabwino ndi chisoti cha ulemu kwa mwamuna wake,*+ koma mkazi wochita zinthu zochititsa manyazi ali ngati chowoletsa mafupa a mwamunayo.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:4 Nsanja ya Olonda,1/15/2003, ptsa. 29-30
4 Mkazi wabwino ndi chisoti cha ulemu kwa mwamuna wake,*+ koma mkazi wochita zinthu zochititsa manyazi ali ngati chowoletsa mafupa a mwamunayo.+