Miyambo 17:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Wantchito wochita zinthu mozindikira, adzalamulira mwana wa mbuye wake amene amachita zinthu zochititsa manyazi,+ ndipo adzalandira nawo cholowa pamodzi ndi ana a mbuye wake.+
2 Wantchito wochita zinthu mozindikira, adzalamulira mwana wa mbuye wake amene amachita zinthu zochititsa manyazi,+ ndipo adzalandira nawo cholowa pamodzi ndi ana a mbuye wake.+