Miyambo 18:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mawu a munthu wonenera ena zoipa ali ngati zinthu zofunika kuzimeza msangamsanga,+ zimene zimatsikira mkatikati mwa mimba.+
8 Mawu a munthu wonenera ena zoipa ali ngati zinthu zofunika kuzimeza msangamsanga,+ zimene zimatsikira mkatikati mwa mimba.+