Mlaliki 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ine ndinanena mumtima mwanga+ kuti: “Mulungu woona adzaweruza munthu wolungama ndi munthu woipa,+ pakuti iye ali ndi nthawi yochitira chinthu chilichonse ndiponso yokhudza ntchito iliyonse.”+ Mlaliki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:17 Nsanja ya Olonda,10/1/1999, tsa. 14
17 Ine ndinanena mumtima mwanga+ kuti: “Mulungu woona adzaweruza munthu wolungama ndi munthu woipa,+ pakuti iye ali ndi nthawi yochitira chinthu chilichonse ndiponso yokhudza ntchito iliyonse.”+