Mlaliki 5:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Komanso, masiku onse a moyo wake amadya chakudya chake mu mdima ndi kusautsika mtima kwakukulu,+ amadwala, ndiponso amakhala ndi nkhawa. Mlaliki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:17 Nsanja ya Olonda,5/15/1998, tsa. 5
17 Komanso, masiku onse a moyo wake amadya chakudya chake mu mdima ndi kusautsika mtima kwakukulu,+ amadwala, ndiponso amakhala ndi nkhawa.