19 Komanso, munthu aliyense amene Mulungu woona wam’patsa chuma ndiponso zinthu zambiri,+ ndiye kuti wamulola kuti adye kuchokera pa zinthuzo.+ Wamulolanso kuti alandire mphoto yake ndi kusangalala chifukwa cha ntchito yake imene amaigwira mwakhama.+ Imeneyi ndi mphatso yochokera kwa Mulungu.+