26 Ndipo izi n’zimene ndinapeza: Mkazi amene ali ngati ukonde wosakira nyama, amene mtima wake uli ngati khoka, amene manja ake ali ngati unyolo,+ ndi wowawa kuposa imfa.+ Munthu amakhala wabwino pamaso pa Mulungu woona akapulumuka kwa mkaziyo, koma amachimwa akagwidwa naye.+