Nyimbo ya Solomo 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Maluwa ayamba kuoneka m’dziko,+ nthawi yodulira mpesa+ yakwana, ndipo m’dziko lathu mukumveka kulira kwa njiwa.+
12 Maluwa ayamba kuoneka m’dziko,+ nthawi yodulira mpesa+ yakwana, ndipo m’dziko lathu mukumveka kulira kwa njiwa.+