4 “Ndiwe wokongola kwabasi,+ wokondedwa wanga. Ndiwe chiphadzuwa. Maso ako ali ngati maso a njiwa+ munsalu yako yophimba kumutuyo.+ Tsitsi lako likuoneka ngati gulu la mbuzi+ zimene zikudumphadumpha potsetsereka kuchokera kudera lamapiri la Giliyadi.+