Nyimbo ya Solomo 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 M’kamwa mwake ndi mokoma kwambiri ndipo chilichonse mwa iye n’chosiririka.+ Ameneyu ndiye wachikondi wanga ndipo ameneyutu ndiye wokondedwa wanga, inu ana aakazi a ku Yerusalemu.”
16 M’kamwa mwake ndi mokoma kwambiri ndipo chilichonse mwa iye n’chosiririka.+ Ameneyu ndiye wachikondi wanga ndipo ameneyutu ndiye wokondedwa wanga, inu ana aakazi a ku Yerusalemu.”