Yesaya 7:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Zinthu zimenezi zidzabwera zonse n’kutera m’zigwa* zokhala ndi maphompho, m’ming’alu ya m’matanthwe, patchire lonse lokhala ndi zitsamba zaminga, ndiponso pamalo onse omwetserapo ziweto.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:19 Yesaya 1, tsa. 110
19 Zinthu zimenezi zidzabwera zonse n’kutera m’zigwa* zokhala ndi maphompho, m’ming’alu ya m’matanthwe, patchire lonse lokhala ndi zitsamba zaminga, ndiponso pamalo onse omwetserapo ziweto.+