Yesaya 15:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mfuu yamveka m’dziko lonse la Mowabu.+ Kufuula kwake kwamveka mpaka ku Egilaimu. Kufuula kwake kwamveka mpaka ku Beere-elimu,
8 Mfuu yamveka m’dziko lonse la Mowabu.+ Kufuula kwake kwamveka mpaka ku Egilaimu. Kufuula kwake kwamveka mpaka ku Beere-elimu,