Yesaya 17:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye sadzayang’ana maguwa a nsembe,+ omwe ndi ntchito ya manja ake.+ Sadzayang’anitsitsa zimene zala zake zapanga, kaya mizati yopatulika kapena maguwa ofukizirapo zonunkhira.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:8 Yesaya 1, ptsa. 196-197
8 Iye sadzayang’ana maguwa a nsembe,+ omwe ndi ntchito ya manja ake.+ Sadzayang’anitsitsa zimene zala zake zapanga, kaya mizati yopatulika kapena maguwa ofukizirapo zonunkhira.+