Yesaya 22:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iwe unali mzinda wodzaza ndi chipwirikiti, waphokoso, komanso unali mudzi wokondwa.+ Anthu ako amene aphedwa, sanaphedwe ndi lupanga ndiponso sanaphedwe kunkhondo.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:2 Yesaya 1, ptsa. 233-234
2 Iwe unali mzinda wodzaza ndi chipwirikiti, waphokoso, komanso unali mudzi wokondwa.+ Anthu ako amene aphedwa, sanaphedwe ndi lupanga ndiponso sanaphedwe kunkhondo.+