2 Zidzakhala chimodzimodzi kwa anthuwo ndi kwa wansembe, kwa wantchito ndi kwa mbuye wake, kwa wantchito wamkazi ndi kwa mbuye wake wamkazi, kwa wogula ndi kwa wogulitsa, kwa wobwereketsa ndi kwa wobwereka, kwa wolandira chiwongoladzanja ndi kwa wopereka chiwongoladzanja.+