Yesaya 24:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 N’chifukwa chake iwo adzalemekeze Yehova+ m’chigawo cha kuwala.*+ M’zilumba zakunyanja adzalemekeza dzina la Yehova,+ Mulungu wa Isiraeli. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:15 Nsanja ya Olonda,12/1/2006, tsa. 11 Yesaya 1, ptsa. 264-266
15 N’chifukwa chake iwo adzalemekeze Yehova+ m’chigawo cha kuwala.*+ M’zilumba zakunyanja adzalemekeza dzina la Yehova,+ Mulungu wa Isiraeli.